Danieli 4:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano ine Nebukadinezara ndikutamanda, kukweza ndi kulemekeza Mfumu yakumwamba,+ chifukwa ntchito zake zonse ndi zogwirizana ndi choonadi, njira zake ndi zolungama+ ndiponso amatha kutsitsa anthu onyada.”+ Yakobo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli. Nʼchifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikuza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+
37 Tsopano ine Nebukadinezara ndikutamanda, kukweza ndi kulemekeza Mfumu yakumwamba,+ chifukwa ntchito zake zonse ndi zogwirizana ndi choonadi, njira zake ndi zolungama+ ndiponso amatha kutsitsa anthu onyada.”+
6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli. Nʼchifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikuza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+