-
Ezekieli 26:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Anthu omwe akukhala mʼmidzi yako imene ili kunja kwa mzindawu adzawapha ndi lupanga. Iye adzamanga mpanda womenyerapo nkhondo komanso malo okwera omenyerapo nkhondo kuti amenyane nawe ndipo adzakuukira ndi chishango chachikulu. 9 Mfumuyo idzagumula mpanda wako ndi chida chogumulira,* ndipo idzagwetsa nsanja zako pogwiritsa ntchito nkhwangwa zake.*
-