Yesaya 60:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyo, udzaona zimenezi ndipo nkhope yako idzasangalala.+Mtima wako udzagunda mwamphamvu ndipo udzasangalala kwambiri,Chifukwa chuma chamʼnyanja adzachibweretsa kwa iwe.Katundu wa mitundu ya anthu adzabwera kwa iwe.+
5 Pa nthawi imeneyo, udzaona zimenezi ndipo nkhope yako idzasangalala.+Mtima wako udzagunda mwamphamvu ndipo udzasangalala kwambiri,Chifukwa chuma chamʼnyanja adzachibweretsa kwa iwe.Katundu wa mitundu ya anthu adzabwera kwa iwe.+