Ezekieli 20:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma ndidzachotsa anthu opanduka komanso amene akundichimwira pakati panu.+ Chifukwa ndidzawatulutsa mʼdziko limene akukhalamo monga alendo, koma sadzalowa mʼdziko la Isiraeli,+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’
38 Koma ndidzachotsa anthu opanduka komanso amene akundichimwira pakati panu.+ Chifukwa ndidzawatulutsa mʼdziko limene akukhalamo monga alendo, koma sadzalowa mʼdziko la Isiraeli,+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’