-
1 Mafumu 9:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Koma inuyo ndi ana anu mukadzasiya kunditsatira nʼkusiyanso kutsatira malamulo anga amene ndakupatsani komanso mukadzapita kukatumikira milungu ina ndi kuigwadira,+ 7 ndidzachotsa Aisiraeli mʼdziko limene ndawapatsa+ ndipo nyumba imene ndaiyeretsa chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga.+ Aisiraeli adzatonzedwa ndi kunyozedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+
-