Yesaya 32:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa nsanja yokhala ndi mpanda wolimba yasiyidwa.Mzinda waphokoso wasiyidwa.+ Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka chipululu mpaka kalekale.Zasanduka malo amene abulu amʼtchire akusangalalako,Komanso malo odyetserako ziweto,+
14 Chifukwa nsanja yokhala ndi mpanda wolimba yasiyidwa.Mzinda waphokoso wasiyidwa.+ Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka chipululu mpaka kalekale.Zasanduka malo amene abulu amʼtchire akusangalalako,Komanso malo odyetserako ziweto,+