Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Chifukwa iwo ndi mtundu wopanda nzeru,*

      Ndipo ndi osazindikira.+

  • Yesaya 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ngʼombe yamphongo imadziwa bwino munthu amene anaigula,

      Ndipo bulu amadziwa chinthu chimene mbuye wake amamudyetseramo.

      Koma Isiraeli sakundidziwa,*+

      Anthu anga sachita zinthu mozindikira.”

  • Yeremiya 4:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Anthu anga ndi opusa.+

      Iwo saganizira za ine.

      Ndi ana opusa ndipo samvetsa zinthu.

      Amaoneka ochenjera* akamachita zoipa,

      Koma sadziwa kuchita zabwino.”

  • Hoseya 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Anthu anga adzakhalitsidwa chete* chifukwa cha kusadziwa.

      Popeza iwo akana kundidziwa,+

      Inenso ndidzawakana kuti asamanditumikire ngati wansembe wanga.

      Komanso chifukwa chakuti iwo aiwala lamulo* la ine Mulungu wawo,+

      Inenso ndidzaiwala ana awo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena