2 Mafumu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼchaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ nʼkutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani+ ndiponso mʼmizinda ya Amedi.+ Yesaya 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Padzakhala msewu waukulu+ wochokera kudziko la Asuri woti mudzadutse anthu ake amene adzatsale,+Ngati mmene zinalili kwa Aisiraeli pamene ankatuluka mʼdziko la Iguputo. Hoseya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwe sudzapitiriza kukhala mʼdziko la Yehova.+Mʼmalomwake Efuraimu adzabwerera ku Iguputo,Ndipo adzadya zinthu zodetsedwa kudziko la Asuri.+
6 Mʼchaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ nʼkutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani+ ndiponso mʼmizinda ya Amedi.+
16 Padzakhala msewu waukulu+ wochokera kudziko la Asuri woti mudzadutse anthu ake amene adzatsale,+Ngati mmene zinalili kwa Aisiraeli pamene ankatuluka mʼdziko la Iguputo.
3 Iwe sudzapitiriza kukhala mʼdziko la Yehova.+Mʼmalomwake Efuraimu adzabwerera ku Iguputo,Ndipo adzadya zinthu zodetsedwa kudziko la Asuri.+