Salimo 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye amaphunzitsa manja anga kumenya nkhondo,Manja anga angathe kukunga uta wakopa.* Salimo 68:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mulungu walamula kuti anthu amuope komanso amupatse ulemu mʼmalo ake opatulika aulemerero.+ Iye ndi Mulungu wa Isiraeli,Amene amapereka mphamvu ndi nyonga kwa anthu.+ Mulungu atamandike.
35 Mulungu walamula kuti anthu amuope komanso amupatse ulemu mʼmalo ake opatulika aulemerero.+ Iye ndi Mulungu wa Isiraeli,Amene amapereka mphamvu ndi nyonga kwa anthu.+ Mulungu atamandike.