Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndidzayeza Yerusalemu ndi chingwe chimene ndinayezera+ Samariya+ ndiponso ndidzamuyeza ndi levulo imene ndinayezera nyumba ya Ahabu.+ Yerusalemu ndidzamʼpukuta mpaka kuyera ngati mmene munthu amapukutira mbale yolowa mpaka kuyera, nʼkuitembenuza.+

  • Yesaya 28:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chilungamo ndidzachisandutsa chingwe choyezera+

      Komanso ndidzachisandutsa chipangizo chosalazira.*+

      Mvula yamatalala idzakokolola malo othawirapo abodza,

      Ndipo madzi adzasefukira pamalo obisalako.

  • Maliro 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova watsimikiza kuti awononge mpanda wa mwana wamkazi wa Ziyoni.+

      Watambasula chingwe choyezera.+

      Sanabweze dzanja lake kuti lisabweretse chiwonongeko.

      Wachititsa kuti malo okwera omenyerapo nkhondo ndi mpanda zilire.

      Zonse pamodzi zachititsidwa kuti zisakhalenso ndi mphamvu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena