Salimo 81:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine Yehova, ndine Mulungu wanu,Amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo.+ Tsegulani kwambiri pakamwa panu ndipo ndidzaikamo chakudya.+ 11 Koma anthu anga sanamvere mawu anga,Isiraeli sanafune kundigonjera.+
10 Ine Yehova, ndine Mulungu wanu,Amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo.+ Tsegulani kwambiri pakamwa panu ndipo ndidzaikamo chakudya.+ 11 Koma anthu anga sanamvere mawu anga,Isiraeli sanafune kundigonjera.+