Yesaya 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Taonani! Yehova akuchotsa anthu onse mʼdziko nʼkulisiya lopanda kanthu.+ Iye wawononga* dzikolo,+ nʼkubalalitsa anthu okhala mmenemo.+
24 Taonani! Yehova akuchotsa anthu onse mʼdziko nʼkulisiya lopanda kanthu.+ Iye wawononga* dzikolo,+ nʼkubalalitsa anthu okhala mmenemo.+