Yesaya 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zimene Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa, wakonza zoti awononge anthuwo,Zidzachitika padziko lonselo.+ Yesaya 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Taonani! Yehova akuchotsa anthu onse mʼdziko nʼkulisiya lopanda kanthu.+ Iye wawononga* dzikolo,+ nʼkubalalitsa anthu okhala mmenemo.+
23 Zimene Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa, wakonza zoti awononge anthuwo,Zidzachitika padziko lonselo.+
24 Taonani! Yehova akuchotsa anthu onse mʼdziko nʼkulisiya lopanda kanthu.+ Iye wawononga* dzikolo,+ nʼkubalalitsa anthu okhala mmenemo.+