Salimo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma munthu amene wasangalala naye* amamukomera mtima kwa moyo wake wonse.+ Munthu akhoza kulira usiku, koma mʼmawa amafuula mosangalala.+ Salimo 103:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye sadzakhalira kutipezera zifukwa nthawi zonse,+Kapena kutisungira mkwiyo mpaka kalekale.+ Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+
5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma munthu amene wasangalala naye* amamukomera mtima kwa moyo wake wonse.+ Munthu akhoza kulira usiku, koma mʼmawa amafuula mosangalala.+
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+