Ekisodo 9:31, 32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pa nthawi imeneyo mbewu za fulakesi* ndi balere zinawonongeka, chifukwa balere anali atakhwima ndipo fulakesi anali atachita maluwa. 32 Koma tirigu* sanawonongeke, chifukwa amakhwima mochedwa.* Ezekieli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo utenge tirigu, balere, nyemba zikuluzikulu, mphodza, mapira ndi sipeloti.* Zonsezo uziike mumphika umodzi kuti zikhale chakudya chako. Pa masiku 390 amene udzakhale ukugonera mbali imodzi uzidzadya chakudya chimenechi.+
31 Pa nthawi imeneyo mbewu za fulakesi* ndi balere zinawonongeka, chifukwa balere anali atakhwima ndipo fulakesi anali atachita maluwa. 32 Koma tirigu* sanawonongeke, chifukwa amakhwima mochedwa.*
9 Ndipo utenge tirigu, balere, nyemba zikuluzikulu, mphodza, mapira ndi sipeloti.* Zonsezo uziike mumphika umodzi kuti zikhale chakudya chako. Pa masiku 390 amene udzakhale ukugonera mbali imodzi uzidzadya chakudya chimenechi.+