Yesaya 41:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+Chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano akuthwa konsekonse. Udzapondaponda mapiri nʼkuwaphwanyaNdipo zitunda udzazisandutsa mankhusu. Amosi 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti,‘“Popeza Damasiko anandigalukira mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapuntha Giliyadi ndi zida zopunthira zachitsulo.+
15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+Chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano akuthwa konsekonse. Udzapondaponda mapiri nʼkuwaphwanyaNdipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.
3 “Yehova wanena kuti,‘“Popeza Damasiko anandigalukira mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapuntha Giliyadi ndi zida zopunthira zachitsulo.+