Yesaya 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzaimba mlandu anthu okhala padziko lapansi chifukwa cha zoipa zawo,+Ndiponso anthu oipa chifukwa cha zolakwa zawo. Ndidzathetsa kunyada kwa anthu odzikuzaNdidzatsitsa kudzikuza kwa olamulira ankhanza.+ Yesaya 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mitundu ya anthu idzachita phokoso ngati mkokomo wa madzi ambiri. Iye adzawadzudzula ndipo iwo adzathawira kutali.Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo mʼmapiriNdiponso ngati udzu wouma wouluzika ndi mphepo yamkuntho.
11 Ndidzaimba mlandu anthu okhala padziko lapansi chifukwa cha zoipa zawo,+Ndiponso anthu oipa chifukwa cha zolakwa zawo. Ndidzathetsa kunyada kwa anthu odzikuzaNdidzatsitsa kudzikuza kwa olamulira ankhanza.+
13 Mitundu ya anthu idzachita phokoso ngati mkokomo wa madzi ambiri. Iye adzawadzudzula ndipo iwo adzathawira kutali.Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo mʼmapiriNdiponso ngati udzu wouma wouluzika ndi mphepo yamkuntho.