Yesaya 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu anthu anga, ndimvereni.Iwe mtundu wanga,+ tchera khutu kwa ine. Chifukwa kwa ine kudzachokera lamulo+Ndipo ndidzachititsa kuti chilungamo changa chikhazikike ngati kuwala ku mitundu ya anthu.+
4 Inu anthu anga, ndimvereni.Iwe mtundu wanga,+ tchera khutu kwa ine. Chifukwa kwa ine kudzachokera lamulo+Ndipo ndidzachititsa kuti chilungamo changa chikhazikike ngati kuwala ku mitundu ya anthu.+