Salimo 33:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Si nzeru kudalira hatchi chifukwa singapulumutse munthu,+Mphamvu zake zochuluka sizingapulumutse munthu Miyambo 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Hatchi amaiphunzitsa pokonzekera tsiku la nkhondo,+Koma Yehova ndi amene amapulumutsa.+
17 Si nzeru kudalira hatchi chifukwa singapulumutse munthu,+Mphamvu zake zochuluka sizingapulumutse munthu