Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 19:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+

  • 2 Mbiri 32:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndiyeno Yehova anatumiza mngelo yemwe anapha msilikali aliyense wamphamvu,+ mtsogoleri ndiponso mkulu wa asilikali aliyense mumsasa wa mfumu ya Asuri, moti mfumuyo inabwerera kwawo mwamanyazi. Kenako inalowa mʼkachisi wa mulungu wake ndipo ena mwa ana ake anaipha ndi lupanga mʼkachisimo.+

  • Yesaya 37:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Ndiyeno mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000. Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena