Maliro 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo ankafunsa amayi awo kuti: “Kodi chakudya ndi vinyo zili kuti?”+ Pamene ankakomoka mʼmabwalo a mzinda ngati munthu amene wavulazidwa,Ndiponso pamene moyo wawo unkachoka ali mʼmanja mwa mayi awo. Zefaniya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chuma chawo chidzatengedwa ndipo nyumba zawo zidzawonongedwa.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wake.+
12 Iwo ankafunsa amayi awo kuti: “Kodi chakudya ndi vinyo zili kuti?”+ Pamene ankakomoka mʼmabwalo a mzinda ngati munthu amene wavulazidwa,Ndiponso pamene moyo wawo unkachoka ali mʼmanja mwa mayi awo.
13 Chuma chawo chidzatengedwa ndipo nyumba zawo zidzawonongedwa.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wake.+