-
Zefaniya 1:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 “Ndidzatambasula dzanja langa nʼkuwononga Yuda,
Ndiponso anthu onse okhala mu Yerusalemu.
Ndidzawononga chilichonse chokhudza Baala+ pamalowa.
Ndidzawononganso ansembe komanso dzina la ansembe a mulungu wachilendo.+
-