Genesis 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Yehova anati: “Ndamva madandaulo ambiri+ akuti machimo a anthu amene akukhala mʼmizinda ya Sodomu ndi Gomora ndi oipa kwambiri.+ Yesaya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imvani mawu a Yehova, inu olamulira ankhanza a ku Sodomu.+ Mvetserani malamulo* a Mulungu wathu, inu anthu a ku Gomora.+ Yuda 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mofanana ndi zimenezi, anthu amʼmizinda ya Sodomu ndi Gomora komanso mizinda yozungulira ankachita chiwerewere* chonyansa kwambiri ndiponso kugonana mʼnjira imene si yachibadwa.+ Anthu amenewa anapatsidwa chilango cha chiwonongeko chosatha*+ ndipo ndi chitsanzo chotichenjeza.
20 Kenako Yehova anati: “Ndamva madandaulo ambiri+ akuti machimo a anthu amene akukhala mʼmizinda ya Sodomu ndi Gomora ndi oipa kwambiri.+
10 Imvani mawu a Yehova, inu olamulira ankhanza a ku Sodomu.+ Mvetserani malamulo* a Mulungu wathu, inu anthu a ku Gomora.+
7 Mofanana ndi zimenezi, anthu amʼmizinda ya Sodomu ndi Gomora komanso mizinda yozungulira ankachita chiwerewere* chonyansa kwambiri ndiponso kugonana mʼnjira imene si yachibadwa.+ Anthu amenewa anapatsidwa chilango cha chiwonongeko chosatha*+ ndipo ndi chitsanzo chotichenjeza.