Salimo 39:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Imvani pemphero langa, inu Yehova,Mvetserani pamene ndikulira kupempha thandizo.+ Musanyalanyaze misozi yanga. Chifukwa ndine mlendo kwa inu,+Mlendo wongodutsa mofanana ndi makolo anga onse.+ Salimo 56:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu mukudziwa bwino za kuthawathawa kwanga.+ Sungani misozi yanga mʼthumba lanu lachikopa.+ Kodi misozi yanga sinalembedwe mʼbuku lanu?+
12 Imvani pemphero langa, inu Yehova,Mvetserani pamene ndikulira kupempha thandizo.+ Musanyalanyaze misozi yanga. Chifukwa ndine mlendo kwa inu,+Mlendo wongodutsa mofanana ndi makolo anga onse.+
8 Inu mukudziwa bwino za kuthawathawa kwanga.+ Sungani misozi yanga mʼthumba lanu lachikopa.+ Kodi misozi yanga sinalembedwe mʼbuku lanu?+