-
Yoswa 10:12, 13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Pa tsiku limene Yehova anapereka Aamori kwa Aisiraeli, mʼpamene Yoswa analankhula ndi Yehova pamaso pa Aisiraeli kuti:
13 Choncho dzuwa linaimadi, ndiponso mwezi sunayende mpaka mtunduwo utalanga adani ake. Kodi sizinalembedwe mʼbuku la Yasari?+ Dzuwa linaima kumwamba pakatikati, ndipo linaimabe choncho pafupifupi maola 24.*
-