Yesaya 43:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ineyo ndi amene ndikufafaniza zolakwa zako*+ chifukwa cha dzina langa,+Ndipo machimo ako sindidzawakumbukira.+ Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+
25 Ineyo ndi amene ndikufafaniza zolakwa zako*+ chifukwa cha dzina langa,+Ndipo machimo ako sindidzawakumbukira.+
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+