Salimo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi imfa yanga ili* ndi phindu lanji? Kodi pali phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+ Kodi fumbi lingakutamandeni?+ Kodi lingalengeze kuti inu ndinu wokhulupirika?+
9 Kodi imfa yanga ili* ndi phindu lanji? Kodi pali phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+ Kodi fumbi lingakutamandeni?+ Kodi lingalengeze kuti inu ndinu wokhulupirika?+