Mlaliki 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse+ komanso salandira mphoto iliyonse,* chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zimaiwalika.+ Mlaliki 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse, chifukwa ku Manda*+ kumene ukupitako kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu kapena nzeru.
5 Chifukwa amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse+ komanso salandira mphoto iliyonse,* chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zimaiwalika.+
10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse, chifukwa ku Manda*+ kumene ukupitako kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu kapena nzeru.