Salimo 30:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwasintha kulira kwanga kuti kukhale kuvina.Mwandivula chiguduli changa ndipo mwandiveka chisangalalo,12 Kuti ndiimbe nyimbo zokutamandani ndipo ndisakhale chete. Inu Yehova Mulungu wanga, ndidzakutamandani mpaka kalekale.
11 Mwasintha kulira kwanga kuti kukhale kuvina.Mwandivula chiguduli changa ndipo mwandiveka chisangalalo,12 Kuti ndiimbe nyimbo zokutamandani ndipo ndisakhale chete. Inu Yehova Mulungu wanga, ndidzakutamandani mpaka kalekale.