2 Mafumu 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Yesaya anati: “Bweretsani keke ya nkhuyu zouma.” Choncho iwo anabweretsadi nʼkuiika pachotupa* chimene Hezekiya anali nacho ndipo anayamba kuchira.+
7 Kenako Yesaya anati: “Bweretsani keke ya nkhuyu zouma.” Choncho iwo anabweretsadi nʼkuiika pachotupa* chimene Hezekiya anali nacho ndipo anayamba kuchira.+