2 Mbiri 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zimenezi zitachitika, anthu ambiri ankabweretsa mphatso kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwino kwambiri kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye ankalemekezedwa ndi anthu a mitundu yonse.
23 Zimenezi zitachitika, anthu ambiri ankabweretsa mphatso kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwino kwambiri kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye ankalemekezedwa ndi anthu a mitundu yonse.