Mika 3:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma mumadana ndi zinthu zabwino+ ndipo mumakonda zinthu zoipa.+Mumasenda khungu la anthu anga nʼkuchotsa mnofu pamafupa awo.+ 3 Mumadyanso mnofu wa anthu anga,+Ndipo mumasenda khungu lawo.Mumaswa mafupa awo nʼkuwaphwanyaphwanya.+Ngati zinthu zimene zaphikidwa mumphika* komanso ngati nyama imene ili mumphika.
2 Koma mumadana ndi zinthu zabwino+ ndipo mumakonda zinthu zoipa.+Mumasenda khungu la anthu anga nʼkuchotsa mnofu pamafupa awo.+ 3 Mumadyanso mnofu wa anthu anga,+Ndipo mumasenda khungu lawo.Mumaswa mafupa awo nʼkuwaphwanyaphwanya.+Ngati zinthu zimene zaphikidwa mumphika* komanso ngati nyama imene ili mumphika.