2 Mbiri 32:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Hezekiya anakhala ndi chuma chambiri ndiponso ulemerero.+ Anamanga nyumba zake zosungiramo+ siliva, golide, miyala yamtengo wapatali, mafuta a basamu, zishango ndiponso zinthu zonse zabwino kwambiri.
27 Hezekiya anakhala ndi chuma chambiri ndiponso ulemerero.+ Anamanga nyumba zake zosungiramo+ siliva, golide, miyala yamtengo wapatali, mafuta a basamu, zishango ndiponso zinthu zonse zabwino kwambiri.