2 Mafumu 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehoyakini mfumu ya Yuda anapita kwa mfumu ya Babulo+ pamodzi ndi mayi ake, atumiki ake, akalonga ake ndi nduna za panyumba yake+ ndipo mfumu ya Babuloyo inamutenga nʼkupita naye ku ukapolo mʼchaka cha 8 cha ufumu wake.+ Danieli 2:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Shadireki,* Misheki* ndi Abedinego+ kuti akhale oyangʼanira ntchito za boma mʼchigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli ankagwira ntchito kunyumba ya mfumu. Danieli 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Belisazara analamula kuti Danieli avekedwe zovala zapepo ndi mkanda wagolide mʼkhosi mwake. Ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+
12 Yehoyakini mfumu ya Yuda anapita kwa mfumu ya Babulo+ pamodzi ndi mayi ake, atumiki ake, akalonga ake ndi nduna za panyumba yake+ ndipo mfumu ya Babuloyo inamutenga nʼkupita naye ku ukapolo mʼchaka cha 8 cha ufumu wake.+
49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Shadireki,* Misheki* ndi Abedinego+ kuti akhale oyangʼanira ntchito za boma mʼchigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli ankagwira ntchito kunyumba ya mfumu.
29 Ndiyeno Belisazara analamula kuti Danieli avekedwe zovala zapepo ndi mkanda wagolide mʼkhosi mwake. Ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+