Yobu 38:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi unali kuti pamene ndinkaika maziko a dziko lapansi?+ Ndiuze ngati ukudziwa mmene zinakhalira. 5 Ndi ndani amene anaika miyezo yake, ngati ukudziwa,Kapena ndi ndani analiyeza ndi chingwe choyezera?
4 Kodi unali kuti pamene ndinkaika maziko a dziko lapansi?+ Ndiuze ngati ukudziwa mmene zinakhalira. 5 Ndi ndani amene anaika miyezo yake, ngati ukudziwa,Kapena ndi ndani analiyeza ndi chingwe choyezera?