Zekariya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Yehova wanena kuti, ‘“Ndidzabwerera ku Yerusalemu nʼkuchitira chifundo mzinda umenewu+ ndipo nyumba yanga idzamangidwa mumzindawu.+ Chingwe choyezera chidzatambasulidwa pa Yerusalemu,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.’
16 Choncho Yehova wanena kuti, ‘“Ndidzabwerera ku Yerusalemu nʼkuchitira chifundo mzinda umenewu+ ndipo nyumba yanga idzamangidwa mumzindawu.+ Chingwe choyezera chidzatambasulidwa pa Yerusalemu,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.’