Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mʼchaka cha 9 cha ufumu wa Zedekiya, mʼmwezi wa 10, pa tsiku la 10 la mweziwo, Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu pamodzi ndi asilikali ake onse.+ Anabwera kudzamenyana ndi anthu amumzindawo ndipo anamanga msasa komanso mpanda kuzungulira mzinda wonsewo.+

  • Yeremiya 32:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pa nthawi imeneyo, asilikali a mfumu ya Babulo anali atazungulira Yerusalemu. Ndipo mneneri Yeremiya anali atamutsekera mʼnyumba imene inali mʼBwalo la Alonda,+ limene linali pafupi ndi nyumba ya mfumu ya Yuda.

  • Yeremiya 39:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Mʼchaka cha 9 cha ulamuliro wa Mfumu Zedekiya ya Yuda, mʼmwezi wa 10, Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo ndi asilikali ake onse anafika ku Yerusalemu nʼkuzungulira mzindawo.+

  • Yeremiya 52:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mʼchaka cha 9 cha ufumu wa Zedekiya, mʼmwezi wa 10, pa tsiku la 10 la mweziwo, Nebukadinezara* mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu pamodzi ndi asilikali ake onse. Anabwera kudzamenyana ndi anthu amumzindawo ndipo anamanga msasa komanso mpanda kuzungulira mzinda wonsewo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena