Mika 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu anthu a ku Lakisi, mangirirani galeta ku gulu la mahatchi.*+ Ndinu amene munayambitsa tchimo la mwana wamkazi wa Ziyoni,*Popeza kugalukira kwa Isiraeli kunapezeka mwa inu.+
13 Inu anthu a ku Lakisi, mangirirani galeta ku gulu la mahatchi.*+ Ndinu amene munayambitsa tchimo la mwana wamkazi wa Ziyoni,*Popeza kugalukira kwa Isiraeli kunapezeka mwa inu.+