Ekisodo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukagula kapolo wa Chiheberi,+ adzakhala kapolo wanu kwa zaka 6, koma mʼchaka cha 7 muzimumasula ndipo azichoka osapereka chilichonse.+ Levitiko 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chaka cha 50 chizidzakhala chopatulika ndipo muzidzalengeza ufulu kwa anthu onse okhala mʼdzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu kwa inu, ndipo aliyense azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+
2 Mukagula kapolo wa Chiheberi,+ adzakhala kapolo wanu kwa zaka 6, koma mʼchaka cha 7 muzimumasula ndipo azichoka osapereka chilichonse.+
10 Chaka cha 50 chizidzakhala chopatulika ndipo muzidzalengeza ufulu kwa anthu onse okhala mʼdzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu kwa inu, ndipo aliyense azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+