-
Genesis 15:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho iye anatenga zonsezi nʼkuzidula pakati ndipo anaika mbali iliyonse moyangʼanizana ndi inzake, koma mbalamezo sanazidule.
-
-
Genesis 15:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Dzuwa litalowa komanso mdima utayamba, ngʼanjo yofuka utsi inaonekera ndipo muuni wamoto unadutsa pakati pa nyama zodulidwazo.
-