Levitiko 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukuthamangitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja, ndipo mizinda yanu idzawonongedwa.+ Yeremiya 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Inu mwaona masoka onse amene ndinagwetsera Yerusalemu+ ndi mizinda yonse ya Yuda. Lero mizinda imeneyi ndi mabwinja okhaokha ndipo palibe amene akukhalamo.+
33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukuthamangitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja, ndipo mizinda yanu idzawonongedwa.+
2 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Inu mwaona masoka onse amene ndinagwetsera Yerusalemu+ ndi mizinda yonse ya Yuda. Lero mizinda imeneyi ndi mabwinja okhaokha ndipo palibe amene akukhalamo.+