Yeremiya 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nenani zimenezi kwa anthu a mitundu ina.Lengezani kuti zimenezi zidzachitikira Yerusalemu.” “Akazitape* akubwera kuchokera kudziko lakutaliNdipo adzalengeza mofuula zimene zidzachitikire mizinda ya Yuda. Yeremiya 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ‘Aisiraeli ndi Ayuda akhala akuchita zoipa zokhazokha pamaso panga kuyambira ali ana.+ Aisiraeli akhala akundikhumudwitsa ndi ntchito za manja awo,’ akutero Yehova.
16 Nenani zimenezi kwa anthu a mitundu ina.Lengezani kuti zimenezi zidzachitikira Yerusalemu.” “Akazitape* akubwera kuchokera kudziko lakutaliNdipo adzalengeza mofuula zimene zidzachitikire mizinda ya Yuda.
30 ‘Aisiraeli ndi Ayuda akhala akuchita zoipa zokhazokha pamaso panga kuyambira ali ana.+ Aisiraeli akhala akundikhumudwitsa ndi ntchito za manja awo,’ akutero Yehova.