Yeremiya 7:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Awa ndi mawu amene Yehova anauza Yeremiya. Iye anamuuza kuti: 2 “Ukaime pageti la nyumba ya Yehova ndipo ukalengeze uthenga uwu, ‘Tamverani mawu a Yehova inu anthu nonse a mu Yuda, amene mumalowa pamageti awa kuti mukalambire Yehova.
7 Awa ndi mawu amene Yehova anauza Yeremiya. Iye anamuuza kuti: 2 “Ukaime pageti la nyumba ya Yehova ndipo ukalengeze uthenga uwu, ‘Tamverani mawu a Yehova inu anthu nonse a mu Yuda, amene mumalowa pamageti awa kuti mukalambire Yehova.