Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 20:2, 3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho anthu anapita kukauza Yehosafati kuti: “Kwabwera chigulu cha anthu kuchokera kuchigawo chakunyanja,* ku Edomu,+ kudzamenyana nanu ndipo ali ku Hazazoni-tamara, kapena kuti ku Eni-gedi.”+ 3 Yehosafati atamva zimenezi anachita mantha ndipo anatsimikiza mumtima mwake kuti afunefune Yehova.+ Choncho analengeza kuti Ayuda onse asale kudya.

  • Esitere 4:15, 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Esitere anayankha Moredikayi kuti: 16 “Pitani mukasonkhanitse Ayuda onse amene ali ku Susani* ndipo musale kudya+ mʼmalo mwa ine. Musadye kapena kumwa kwa masiku atatu,+ masana ndiponso usiku. Inenso ndi atsikana onditumikira tisala kudya. Ngakhale kuti ndi zosemphana ndi lamulo, ndidzapita kwa mfumu ndipo ngati nʼkufa, ndife.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena