Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+ Yeremiya 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndikubweretsera mzinda uwu ndi matauni ake onse masoka onse amene ndinanena, chifukwa anthu ake aumitsa mitima yawo nʼkukana* kumvera mawu anga.’”+
15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+
15 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndikubweretsera mzinda uwu ndi matauni ake onse masoka onse amene ndinanena, chifukwa anthu ake aumitsa mitima yawo nʼkukana* kumvera mawu anga.’”+