Yeremiya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova wanena kuti, ‘Ndikuitana mafuko onse a maufumu a kumpoto.+Iwo adzabwera ndipo aliyense adzakhazikitsa mpando wake wachifumu,Pakhomo la mageti a Yerusalemu.+Iwo adzaukira mpanda wake wonseNdi mizinda yonse ya Yuda.+
15 Yehova wanena kuti, ‘Ndikuitana mafuko onse a maufumu a kumpoto.+Iwo adzabwera ndipo aliyense adzakhazikitsa mpando wake wachifumu,Pakhomo la mageti a Yerusalemu.+Iwo adzaukira mpanda wake wonseNdi mizinda yonse ya Yuda.+