Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 40:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno mkulu wa asilikali olondera mfumuyu anatengera Yeremiya pambali nʼkumuuza kuti: “Yehova Mulungu wako ananeneratu kuti tsoka ili lidzagwera dziko lino

  • Yeremiya 40:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Lero ndikumasula maunyolo amene ali mʼmanja mwako. Ngati ungakonde kupita nane ku Babulo, tiye ndipo ndizikakuyangʼanira. Koma ngati sukufuna kupita nane ku Babulo, usapite. Taona! Dziko lonse lili pamaso pako. Pita kulikonse kumene ungakonde.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena