Yeremiya 38:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ebedi-meleki+ wa ku Itiyopiya, amene anali nduna mʼnyumba ya mfumu, anamva kuti Yeremiya amuponya mʼchitsime. Apa nʼkuti mfumu itakhala pa Geti la Benjamini.+
7 Ebedi-meleki+ wa ku Itiyopiya, amene anali nduna mʼnyumba ya mfumu, anamva kuti Yeremiya amuponya mʼchitsime. Apa nʼkuti mfumu itakhala pa Geti la Benjamini.+