Levitiko 19:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Musamamete ndevu zanu zotsikira mʼmasaya kapena kudula nsonga za ndevu zanu.*+ 28 Musamadzicheke chifukwa cha munthu wakufa,+ ndipo musamadzilembe zizindikiro pakhungu lanu. Ine ndine Yehova. Deuteronomo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu. Musamadzichekecheke+ kapena kumeta nsidze zanu* chifukwa cha anthu akufa.+
27 Musamamete ndevu zanu zotsikira mʼmasaya kapena kudula nsonga za ndevu zanu.*+ 28 Musamadzicheke chifukwa cha munthu wakufa,+ ndipo musamadzilembe zizindikiro pakhungu lanu. Ine ndine Yehova.
14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu. Musamadzichekecheke+ kapena kumeta nsidze zanu* chifukwa cha anthu akufa.+