2 Mafumu 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zitatero, anthu onse, kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu komanso akuluakulu a magulu a asilikali, anathawira ku Iguputo,+ chifukwa ankaopa Akasidi.+ Yeremiya 42:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ponena kuti, “Ayi, mʼmalomwake tipita kudziko la Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya. Ife tizikakhala kumeneko,” Yeremiya 43:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anapita mʼdziko la Iguputo chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo anakafika ku Tahapanesi.+
26 Zitatero, anthu onse, kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu komanso akuluakulu a magulu a asilikali, anathawira ku Iguputo,+ chifukwa ankaopa Akasidi.+
14 ponena kuti, “Ayi, mʼmalomwake tipita kudziko la Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya. Ife tizikakhala kumeneko,”